Numeri 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Balamu anauza Balaki kuti: “Mumange maguwa ansembe okwanira 7+ pamalo ano. Mukatero mundikonzere ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.”
23 Kenako Balamu anauza Balaki kuti: “Mumange maguwa ansembe okwanira 7+ pamalo ano. Mukatero mundikonzere ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.”