Numeri 23:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nthawi yomweyo Balaki anachita zimene Balamu anamuuza. Kenako Balaki ndi Balamu anapereka nsembe. Anapereka ngʼombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+
2 Nthawi yomweyo Balaki anachita zimene Balamu anamuuza. Kenako Balaki ndi Balamu anapereka nsembe. Anapereka ngʼombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+