-
Numeri 23:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno Balamu anauza Balaki kuti: “Mukhale pompano pafupi ndi nsembe yanu yopsereza ndipo ine ndichoka. Mwina Yehova alankhula nane ndipo zimene andiuzezo ndikuuzani.” Choncho Balamu anapita pamwamba pa phiri.
-