Numeri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Mulungu anakumana ndi Balamu+ ndipo iye anauza Mulunguyo kuti: “Ndamanga maguwa ansembe 7 mʼmizere, ndipo ndapereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.”
4 Kenako Mulungu anakumana ndi Balamu+ ndipo iye anauza Mulunguyo kuti: “Ndamanga maguwa ansembe 7 mʼmizere, ndipo ndapereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.”