Numeri 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anauza Balamu+ zoti akanene.* Kenako anamuuza kuti: “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze mawu amenewa.”
5 Yehova anauza Balamu+ zoti akanene.* Kenako anamuuza kuti: “Bwerera kwa Balaki, ukamuuze mawu amenewa.”