Numeri 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere? Ndipo ndingathe bwanji kuitanira tsoka anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka?+
8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere? Ndipo ndingathe bwanji kuitanira tsoka anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka?+