Numeri 23:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Balaki anauza Balamu kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandichitira zimenezi? Ndakubweretsani kuno kuti mudzatemberere adani anga, koma inu mwawadalitsa.”+
11 Kenako Balaki anauza Balamu kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwandichitira zimenezi? Ndakubweretsani kuno kuti mudzatemberere adani anga, koma inu mwawadalitsa.”+