Numeri 23:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Balaki anauza Balamu kuti: “Tiyeni tipite kumalo ena kumene mungathe kuwaona anthuwo. Simukaona onse, koma mukangoona ochepa. Mukatemberere amenewo.”+
13 Balaki anauza Balamu kuti: “Tiyeni tipite kumalo ena kumene mungathe kuwaona anthuwo. Simukaona onse, koma mukangoona ochepa. Mukatemberere amenewo.”+