-
Numeri 23:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno Balamu anauza Balaki kuti: “Mukhale pano, pafupi ndi nsembe yanu yopserezayi, koma ine ndikukalankhula ndi Mulungu uko.”
-