-
Numeri 23:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Choncho Balamu anabwerera kwa Balaki, ndipo anamupeza akudikirira pafupi ndi nsembe yake yopsereza, akalonga a ku Mowabu ali naye limodzi. Ndiyeno Balaki anafunsa Balamu kuti: “Kodi Yehova wanena chiyani?”
-