Numeri 23:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera. Ndimvetsere, iwe mwana wa Zipori.
18 Kenako Balamu anayambanso kulankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Nyamuka, Balaki iwe, tamvera. Ndimvetsere, iwe mwana wa Zipori.