Numeri 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Balamu anayankha Balaki kuti: “Kodi sindinakuuzeni kuti, ‘Ndichita zonse zimene Yehova wanenaʼ?”+