Numeri 24:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Balamu atakweza maso ake nʼkuona Aisiraeli ali mʼmisasa mogwirizana ndi mafuko awo,+ mzimu wa Mulungu unafika pa iye.+
2 Balamu atakweza maso ake nʼkuona Aisiraeli ali mʼmisasa mogwirizana ndi mafuko awo,+ mzimu wa Mulungu unafika pa iye.+