Numeri 24:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzamuona, koma osati panopa;Ndidzamupenya, koma osati posachedwa. Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+ Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:17 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 53, 318 Nsanja ya Olonda,5/15/2005, tsa. 17
17 Ndidzamuona, koma osati panopa;Ndidzamupenya, koma osati posachedwa. Nyenyezi+ idzatuluka mwa Yakobo,Ndodo yachifumu+ idzatuluka mu Isiraeli.+ Ndipo iye adzaphwanyadi chipumi cha Mowabu+Ndi mitu ya asilikali onse ankhanza.