-
Numeri 25:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Gwira onse amene akutsogolera anthuwo, ndipo uwaphe nʼkuwapachika pamtengo pamaso pa Yehova dzuwa likuswa mtengo. Uchite zimenezo kuti mkwiyo wa Yehova umene wayakira Aisiraeli uchoke.”
-