-
Numeri 25:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Dzina la mwamuna wa Chiisiraeli, amene anaphedwa limodzi ndi mkazi wa Chimidiyani uja linali Zimiri mwana wa Salu, ndipo anali mtsogoleri wa nyumba ya makolo a fuko la Simiyoni.
-