Numeri 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amenewa anali mabanja a ana a Gadi. Amuna onse amene anawerengedwa analipo 40,500.+