Numeri 26:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi. Mkazi wa Levi anamuberekera mwana ameneyu ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mchemwali wawo Miriamu.+
59 Mkazi wa Amuramu anali Yokebedi,+ mwana wa Levi. Mkazi wa Levi anamuberekera mwana ameneyu ku Iguputo. Yokebedi anaberekera Amuramu ana awa: Aroni, Mose ndi mchemwali wawo Miriamu.+