-
Numeri 26:63Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
63 Awa ndi anthu amene Mose ndi wansembe Eleazara anawawerenga pakati pa Aisiraeli. Anawawerengera mʼchipululu cha Mowabu, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, kufupi ndi Yeriko.
-