Numeri 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Ana aakazi a Tselofekadi akunena zoona. Uwapatsedi malo kuti akhale cholowa chawo pakati pa azichimwene a bambo awo. Cholowa cha bambo awocho chikhale chawo.+
7 “Ana aakazi a Tselofekadi akunena zoona. Uwapatsedi malo kuti akhale cholowa chawo pakati pa azichimwene a bambo awo. Cholowa cha bambo awocho chikhale chawo.+