-
Numeri 27:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Musankhe munthu woti akhale mtsogoleri wawo pa zinthu zonse, woti aziwatsogolera pa zochita zawo zonse, kuti gulu la Yehova lisakhale ngati nkhosa zopanda mʼbusa.”
-