-
Numeri 28:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Muziperekanso mbuzi yaingʼono kuti ikhale nsembe yamachimo kwa Yehova, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yachakumwa.
-