-
Numeri 28:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Pa tsiku loyamba la chikondwererocho muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa pa tsikuli.
-