-
Numeri 28:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Muzipereka nsembe zimenezi limodzi ndi nsembe zake zambewu. Ngʼombe yamphongo iliyonse muziipereka limodzi ndi ufa wosalala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Nkhosa yamphongoyo muziipereka limodzi ndi ufa wokwana magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa. Ufawo uzikhala wothira mafuta.+
-