-
Numeri 28:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Pa mwana wa nkhosa wamphongo aliyense pa ana a nkhosa 7 amenewo, muziperekanso ufa wokwana gawo limodzi mwa magawo 10 a muyezo wa efa.
-