Numeri 28:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Muzipereka nsembe zimenezi mofanana tsiku lililonse kwa masiku 7. Muzizipereka monga chakudya, nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova. Muziipereka limodzi ndi nsembe yopsereza ya nthawi zonse komanso nsembe yake yachakumwa.
24 Muzipereka nsembe zimenezi mofanana tsiku lililonse kwa masiku 7. Muzizipereka monga chakudya, nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* kwa Yehova. Muziipereka limodzi ndi nsembe yopsereza ya nthawi zonse komanso nsembe yake yachakumwa.