-
Numeri 28:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Muziperekanso nsembe yake yambewu ya ufa wosalala wothira mafuta. Ufawo uzikhala wokwana magawo atatu mwa magawo 10 a muyezo wa efa pa ngʼombe yamphongo iliyonse. Pa nkhosa yamphongo imodziyo, muzipereka ufa wokwana magawo awiri mwa magawo 10 a muyezo wa efa.
-