Numeri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Muziperekanso mbuzi yaingʼono imodzi monga nsembe yamachimo. Muziipereka kuwonjezera pa nsembe yamachimo pa tsiku lophimba machimo,+ ndi nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe zake zambewu ndiponso zachakumwa.
11 Muziperekanso mbuzi yaingʼono imodzi monga nsembe yamachimo. Muziipereka kuwonjezera pa nsembe yamachimo pa tsiku lophimba machimo,+ ndi nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe zake zambewu ndiponso zachakumwa.