-
Numeri 29:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Popereka ngʼombe zamphongo, nkhosa zamphongo ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu ndi nsembe zake zachakumwa, mogwirizana ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.
-