-
Numeri 29:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Popereka ngʼombe zamphongo, nkhosa zamphongo ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu ndi nsembe zake zachakumwa, mogwirizana ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse la nsembezi.
-