Numeri 30:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova kapena akachita lumbiro+ lodzimana, asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Azichita zonse zimene walonjezazo.+
2 Munthu akalonjeza+ kwa Yehova kapena akachita lumbiro+ lodzimana, asalephere kukwaniritsa mawu ake.+ Azichita zonse zimene walonjezazo.+