Numeri 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ngati bambo ake amukaniza atamva zimene walonjeza kapena lumbiro lake lodzimana, malonjezowo akhale opanda ntchito. Yehova adzamukhululukira chifukwa bambo ake anamukaniza.+
5 Koma ngati bambo ake amukaniza atamva zimene walonjeza kapena lumbiro lake lodzimana, malonjezowo akhale opanda ntchito. Yehova adzamukhululukira chifukwa bambo ake anamukaniza.+