Numeri 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma mwamuna wake akamukaniza pa tsiku limene wamva zimene analonjezazo, ndiye kuti wafafaniza lonjezo kapena lumbiro limene mkaziyo anachita mosaganiza bwino+ ndipo Yehova adzamukhululukira mkaziyo. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 30:8 Nsanja ya Olonda,8/1/2004, tsa. 27
8 Koma mwamuna wake akamukaniza pa tsiku limene wamva zimene analonjezazo, ndiye kuti wafafaniza lonjezo kapena lumbiro limene mkaziyo anachita mosaganiza bwino+ ndipo Yehova adzamukhululukira mkaziyo.