Numeri 30:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma mwamuna wake akafafaniza malonjezowo pa tsiku limene wamva zimene mkaziyo analonjeza kapena malumbiro ake odzimana amene anachita, malonjezowo azikhala opanda ntchito.+ Mwamuna wake wawafafaniza ndipo Yehova adzamukhululukira mkaziyo.
12 Koma mwamuna wake akafafaniza malonjezowo pa tsiku limene wamva zimene mkaziyo analonjeza kapena malumbiro ake odzimana amene anachita, malonjezowo azikhala opanda ntchito.+ Mwamuna wake wawafafaniza ndipo Yehova adzamukhululukira mkaziyo.