Numeri 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amene anaphedwawo akuphatikizapo mafumu 5 a Chimidiyani. Mafumuwo anali Evi, Rekemu, Zuri, Hura ndi Reba. Komanso anapha Balamu+ mwana wa Beori ndi lupanga.
8 Anthu amene anaphedwawo akuphatikizapo mafumu 5 a Chimidiyani. Mafumuwo anali Evi, Rekemu, Zuri, Hura ndi Reba. Komanso anapha Balamu+ mwana wa Beori ndi lupanga.