-
Numeri 31:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 “Iweyo ndi wansembe Eleazara ndi atsogoleri a gululo, muwerenge zinthu zonse zimene akatenga kunkhondo. Muwerenge anthu ndi ziweto zomwe.
-