-
Numeri 31:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Pa zinthu zimene zaperekedwa kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 500 zilizonse, pa anthu, ngʼombe, abulu ndi nkhosa kuti zikhale msonkho woperekedwa kwa Yehova.
-