Numeri 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nʼzimenenso makolo anu anachita ku Kadesi-barinea, nditawatuma kuti akafufuze dziko.+