Numeri 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo atafika kuchigwa cha Esikolo*+ nʼkuliona dzikolo, anafooketsa Aisiraeli kuti asakalowe mʼdziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+
9 Iwo atafika kuchigwa cha Esikolo*+ nʼkuliona dzikolo, anafooketsa Aisiraeli kuti asakalowe mʼdziko limene Yehova anatsimikiza mtima kuwapatsa.+