Numeri 32:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ifeyo tikonzeka kuti tikamenye nkhondo+ ndipo tikhala patsogolo pa Aisiraeli mpaka titakawafikitsa kumalo awo. Koma ana athu tiwasiya mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kuti tiwateteze kwa anthu a dziko lino.
17 Koma ifeyo tikonzeka kuti tikamenye nkhondo+ ndipo tikhala patsogolo pa Aisiraeli mpaka titakawafikitsa kumalo awo. Koma ana athu tiwasiya mʼmizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri kuti tiwateteze kwa anthu a dziko lino.