Numeri 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Komanso ngati aliyense wa inu atatenga zida zake zankhondo nʼkuwoloka Yorodano pamaso pa Yehova, mpaka atathamangitsa adani ake pamaso pake,+
21 Komanso ngati aliyense wa inu atatenga zida zake zankhondo nʼkuwoloka Yorodano pamaso pa Yehova, mpaka atathamangitsa adani ake pamaso pake,+