Numeri 32:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiye mukhoza kumanga mizinda ya ana anu ndi makola a ziweto zanu.+ Koma muchitedi zimene mwalonjeza.”
24 Ndiye mukhoza kumanga mizinda ya ana anu ndi makola a ziweto zanu.+ Koma muchitedi zimene mwalonjeza.”