Numeri 32:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Beti-nimira+ ndi Beti-harana.+ Mizinda imeneyi inali ndi mipanda yolimba kwambiri komanso inali ndi makola a ziweto amiyala.
36 Beti-nimira+ ndi Beti-harana.+ Mizinda imeneyi inali ndi mipanda yolimba kwambiri komanso inali ndi makola a ziweto amiyala.