Numeri 32:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nebo,+ Baala-meoni,+ ndi Sibima. Mayina a mizindayi anawasintha, nʼkuipatsa mayina ena atsopano.