Numeri 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yairi mwana wa Manase anaukira Aamori nʼkulanda midzi yawo ingʼonoingʼono. Midzi imeneyi anayamba kuitchula kuti Havoti-yairi.*+
41 Yairi mwana wa Manase anaukira Aamori nʼkulanda midzi yawo ingʼonoingʼono. Midzi imeneyi anayamba kuitchula kuti Havoti-yairi.*+