-
Numeri 32:42Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
42 Noba nayenso anaukira nʼkulanda mzinda wa Kenati ndi midzi yake yozungulira. Mzindawo anaupatsa dzina lake, loti Noba.
-