Numeri 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mose ankalemba malo amene ankanyamukira ulendo uliwonse mogwirizana ndi zimene Yehova anamulamula. Awa ndi maulendo amene anayenda kuchokera kumalo ena kukafika kumalo ena:+
2 Mose ankalemba malo amene ankanyamukira ulendo uliwonse mogwirizana ndi zimene Yehova anamulamula. Awa ndi maulendo amene anayenda kuchokera kumalo ena kukafika kumalo ena:+