Numeri 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako ananyamuka ku Sukoti nʼkukamanga msasa ku Etamu,+ pafupi ndi chipululu.