Numeri 33:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Tsopano mfumu ya ku Aradi+ ya Chikanani, imene inkakhala ku Negebu mʼdziko la Kanani, inamva kuti Aisiraeli akubwera.
40 Tsopano mfumu ya ku Aradi+ ya Chikanani, imene inkakhala ku Negebu mʼdziko la Kanani, inamva kuti Aisiraeli akubwera.