Numeri 33:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Anapitiriza kukhala mumsasa pafupi ndi Yorodano, kuyambira ku Beti-yesimoti mpaka ku Abele-sitimu,+ mʼchipululu cha Mowabu.
49 Anapitiriza kukhala mumsasa pafupi ndi Yorodano, kuyambira ku Beti-yesimoti mpaka ku Abele-sitimu,+ mʼchipululu cha Mowabu.